Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

Banja la Kaini ndi Mbewu ya mzimayi


Listen Later

Genesis 4:17-26, ikukamba za banja la Kaini komanso kubweresa poyera kupitirira kwa kusamvera kwa Kaini ndi mtundu wake wonse. Izi zili chomwecho pomwe tikuwona Lameki akukwatira akazi awiri motsutsana ndi dongosolo la ukwati lomwe Mulungu analikhadzikitsa kuti mwamuna akuyenera kukwatira mkazi m'modzi. Panthawi yomweyo tikuwonanso zokhuza mbewu ya mzimayi yomwe ikubwera kudzera mwa Seti yemwe akubadwa ku banja la Adamu ndipo Seti akulowa m'malo mwa Abele yemwe Kaini anamupha.


Genesis 4:17-26, is discussing the family of Cain and continuing to bring to light the ungodly actions of Cain and his descendants when we see La'mech marrying two wives which is against God's marriage order which says that a man is to marry one wife. It is also discussing the seed of a woman where we see the birth of Seth to the family of Adam who is now replacing Abel who Cain killed. 

...more
View all episodesView all episodes
Download on the App Store

Chiphunzitso Choona | Sound DoctrineBy Gospel Life


More shows like Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

View all
Gospel Life | Malawi, Missions, and More by Josh Hutchens & Isaac Dzimbiri | Gospel Life

Gospel Life | Malawi, Missions, and More

12 Listeners