Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

Imfa, Chiwukitso komanso Mapemphero a Yesu Khristu Tsopanolingo


Listen Later

Oyera mtima apirira muchikhulupiriro chawo chifukwa imfa ya Yesu yachotsa chostutsa china chilichonse komanso mlandu uliwonse otsutsana ndi sosakhidwa a Mulungu. Chiukitso cha Yesu ndi chitsimikizo cha chikhulupiriro chathu komanso mpemphero ake opemperera oyera mtima amatsimikizira kuti chikhulupiriro cho sichifowoka.

Preacher: Isaac Dzimbiri

Class: Kudzama Choonadi
Series: Kupirira kwa Oyera Mtima Chikhulupiriro Chawo

...more
View all episodesView all episodes
Download on the App Store

Chiphunzitso Choona | Sound DoctrineBy Gospel Life


More shows like Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

View all
Gospel Life | Malawi, Missions, and More by Josh Hutchens & Isaac Dzimbiri | Gospel Life

Gospel Life | Malawi, Missions, and More

12 Listeners