Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

Mtima wa munthu/A human heart


Listen Later

Mateyu 5:8 ikutithandizira kumvetsetsa lingaliro la malo

opangira katundu. Malo opangira katundu ndi komwe tingapezeko akupanga katundu. Ophunzitsa baibulo odziwika wina ananena kuti, mtima wa munthu ndi malo opangira katundu. Koma katundu wake ndi wotani? Mtima wa munthu ndi malo opangira mafano. Mtima wa munthu nthawi zonse umapanga zinthu za tsopano ndi
kumapembeza zoterozo. Koma baibulo limanena kuti munthu ndi wa padera, mulungu analenga munthu muchifanizo chake. Cholinga chakuti munthu adzilamulira zinthu pansi paulamulilo wa mulungu. Komanso adzimupembeza. Koma m’malo mwake munthu akusankha kupembeza mafano. Buku la Mateyu 5:8 tikulimbikitsidwa kuti tilolere mulungu kutipatsa mtima ofuna kupembeza mulungu. Ndipo akutilonjeza kuti iye ndiwopezekeratu. Tsopano tidziwe kuti mawu a mulungu ndi mawu a munthu ndi osiyana. Munthu amalephera kukwaniritsa zomwe alonjeza chifukwa alibe kuthekera. Koma
mulungu akalonjeza kwa iye zili chimozimozi kuti zachitika kale, ndi chifukwa tiyenera kumudalira.  

Matthew 5:8 helps us to understand the concept of a

factory. A factory is a place where goods are produced. One famous bible scholar said that a human heart is a factory. Now, what is it that the human heart is producing? In simple terms a human heart is a factory for idols. A human heart is constantly making new things to worship. But the bible tells us that humans
are unique, we were created in the image of God, to Reflect his authority and to be in a relationship with him which is described as worship. But as a result, our corrupted hearts always want to worship idols. We have traded worshiping the one true God to worshiping idols. But the book of Matthew 5:8 is encouraging us
to pursue God and promises that we’ll find him and one day we’ll see him in his full glory. Now, the word of God is not like the words of a human being. A human being can make a promise but later on fail to fulfill the promise due to circumstances.
But that is not the same with God. When God has promised something, it is as good as done. So, we can trust that he will keep his promises.

...more
View all episodesView all episodes
Download on the App Store

Chiphunzitso Choona | Sound DoctrineBy Gospel Life


More shows like Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

View all
Gospel Life | Malawi, Missions, and More by Josh Hutchens & Isaac Dzimbiri | Gospel Life

Gospel Life | Malawi, Missions, and More

12 Listeners