
Sign up to save your podcasts
Or


Monga ana womvera wosadzifanizitsanso ndi zilakolako zakale, pokhala wosadziwa inu: Komatu monga Iye wakuyitana inu ali woyera mtima, khalani inunso woyera mtima m’makhalidwe anu onse: Popeza kwalembedwa, mudzikhala woyera mtima, pakuti Ine ndine woyera mtima:
(1Pe 1:14-16)
By John Joseph MatandikaMonga ana womvera wosadzifanizitsanso ndi zilakolako zakale, pokhala wosadziwa inu: Komatu monga Iye wakuyitana inu ali woyera mtima, khalani inunso woyera mtima m’makhalidwe anu onse: Popeza kwalembedwa, mudzikhala woyera mtima, pakuti Ine ndine woyera mtima:
(1Pe 1:14-16)