Chuma mzikho zadothi

Chotitsogolera


Listen Later

Musaganize kuti ndidadza Ine kudzapasula chilamulo kapena aneneri; sindinadza kupasula koma kukwaniritsa. Pakuti indetu ndinena kwa inu, Kufikira litapitirira thambo ndi dziko, kalemba kakang’ono kamodzi kapena kasonga kake kamodzi sikadzachoka kuchilamulo, kufikira zitachitidwa zonse. Chifukwa chake yense womasula limodzi la malamulo amenewa ang’onong’ono, nadzaphunzitsa anthu chomwecho, adzatchulidwa wamng’onong’ono mu Ufumu wa kumwamba; koma yense wochita ndi kuphunzitsa awa, iyeyu adzatchulidwa wa mkulu mu Ufumu wa kumwamba. Pakuti ndinena ndi inu, Ngati chilungamo chanu sichichuluka choposa cha alembi ndi Afarisi, simudzalowa konse mu Ufumu wa kumwamba.

(Mat 5:17-20)

...more
View all episodesView all episodes
Download on the App Store

Chuma mzikho zadothiBy John Joseph Matandika