
Sign up to save your podcasts
Or


Koma pamene wafika Nkhoswe, amene Ine ndidzamtuma kwa inu kuchokera kwa Atate, ndiye Mzimu wa chowonadi amene atuluka kwa Atate, Iyeyu adzandichitira Ine umboni. Ndipo inunso mudzachitira umboni, chifukwa mudali ndi Ine kuyambira pachiyambi.
(Joh 15:26-27)
By John Joseph MatandikaKoma pamene wafika Nkhoswe, amene Ine ndidzamtuma kwa inu kuchokera kwa Atate, ndiye Mzimu wa chowonadi amene atuluka kwa Atate, Iyeyu adzandichitira Ine umboni. Ndipo inunso mudzachitira umboni, chifukwa mudali ndi Ine kuyambira pachiyambi.
(Joh 15:26-27)