Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

Download on the App Store

Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine episodes

  • Kuthekera kwa pemphero/Effectiveness of Prayer

    1 Yohane 5:14-15 pamene talandira chipulumutso timakhala otsimikidzika za moyo wathu wa muyaya umene mulungu analonjeza. Chifukwa cha chitsimikizo chotere timakhulupirira kuti mapemphero athu amayankhidwa ndi mulungu wathu odziwa kuyankha mapemphero athu. Koma kulimba mtima pa moyo wosatha ndi kutsimikizika pa pemphero zimagwira ntchito limodzi. Chifukwa ndi pokhapokha uli ndi kulimba mtima pa moyo wosatha ndi pamene kutsimikidzika mu pemphero kumabwera.


    1 John 5:14-15 when you are saved through faith in Jesus Christ, you become confident that you have eternal life. This confidence in eternal life gives you the assurance of prayer. The God we worship can truly answer prayers and does truly answer prayers. But confidence in eternal life and assurance in prayer truly work together, because its only you have confidence in eternal life can you then be assured that your prayers will be answered.

    37 min
  • Petro anavomereza za Yesu/Peter's confession of Jesus

    Mateyu 16:5-18 Yesu atafunsa ophunzira ake kuti iwo amati Yesu ndi ndani, Petro anayankha kuti "inu ndi Khristu mwana wa Mulungu wa moyo."Ndipo ulendo wa Petro oyenda ndi Khristu unayambika. Kodi ife ngati akhristu timati Yesu ndi ndani? Nkhristu yemwe ndi opulumutsidwa akuyenera kukwanitsa kuyankha funso limeneli ponena kuti "Yesu ndi Khristu mwana wa mulungu ndi ambuye ndi mpulumutsi wa moyo wa aliyense."


    Matthew 16:5-18 Jesus posed a question to his disciples, he asked "who do you say that I am?" Peter answered without any hesitation that 'you are Christ the son of the living God.' As christians today we should be able to answer that question when its posed to us as well. We confidently say that Jesus is the Messiah, truly God and truly man and he the lord and saviour of our lives.

    1 hr 3 min
  • Umboni wa Mulungu/God's Testimony

    1 Yohane 5:6-13 uthenga wabwino omwe Yohane wakhala akulongosola mu buku la 1 Yohane, wakambidwa bwino mu chaputa cha chisanu. Mulungu wa mphamvu zonse akuchitira umboni mwana wake amene ndi Mulungu komanso munthu ndithu. Mulungu atate akuchitira umboni umenewu mu njira zitatu. Njira yoyamba ndi kudzera m'madzi a ubatizo wa Yesu Khristu, magazi a Yesu Khristu pantanda komanso kudzera mzimu. Njira yachiwiri ndi kudzera mu chisankho chimene ife timapanga podzindikira kuti Mulungu sanganame ndipo iye ndi choonadi motero timakhulupirira zonse zomwe amayankhula. Njira yachitatu ndi kudzera mu chipulumutso chimene amapereka kudzera mwa mwana wake Yesu Khristu amene ndi Munthu ndi Mulungu ndithu.


    1 John 5:6-13 the message that John has spoken throughout the whole book of 1 John is clearly explained in chapter 5. The almighty God who sits enthroned gives his testimony of his son being fully Human and fully God. God has done this in three ways. The first way is through the water of Jesus' baptism, his blood at the cross, and the spirit. The second way is through the choice we make realising that God can never lie but that he is the truth. In that sense we believe in all that God tells us because it's true. The third way is through the salvation he gives through his son Jesus Christ who is fully Man and fully God.

    51 min
  • Mphatso ya chipulumutso/The gift of salvation

    2 Petro 1:1-11, aliyense amapatsidwa mphatso ya chipulumutso kudzera mu chikhulupiriro mwa Yesu Khristu. Palibe amapulumutsidwa kudzera mu ntchito zake koma kudzera mu chikhulupiriro chathu mwa Yesu Khristu timapatsidwa mphatso ya chipulumutso. Monga akhristu zinthu zitatu zoyenera kukumbukira,(tapatsidwa Yesu Khristu, tikuyenera kukhala muchikhulupiriro chathu, tikuyenera kuyembekezera chipulumutso chathu).


    2 Peter 1:1-11, everyone is gifted salvation through faith in Jesus Christ. No one is given salvation through his works but through faith in Jesus Christ you are gifted salvation. As christians three things we are to remember, (we are given Jesus Christ, we must practise our faith in Jesus, we must wait faithfully for our salvation).

    41 min
  • Chikhulupiriro/Faith

    1 Yohane 5:1-4, chikhulupiriro chimatipanga ife ana ake a mulungu kukhala ofuna kutsatira malamulo ake. Timaona kuti kutsatira malamulo ake ili ngati njira imodzi yomwe ife timaonetsera chikondi chathu pa mulungu wathu. Timaphunzitsa ena potsatira malamulo a mulungu siwolemetsa konse. Ndichikhulupiriro chathu mwa mulungu ndife olimba kuti sitingagwetsedwe konse.



    1 John 5:1-4, faith make us children of God to have a strong desire to obey his commandments. We see this as an opportunity we have to show our love for him through obedience to him. We teach this to others by following God's commands and that his commandments are not burden.

    30 min
  • Yesu auka mmanda/Jesus is raised from the tomb

    Yohane 20:1-18, Yesu anakwanilitsa zonse zomwe anabwerera kuzachita padziko lapansi. Yesu anakwanitsa kulipira ngongole ya machimo yomwe ife sitikanakwanitsa kulipira patokha. Yesu ali m'manda mulungu anamukitsa kwa akufa pakuti iye anali olungama ndipo sanayenera kuti thupi lake lichite chivundi. Tsopano lino ali kumwamba kwa atate ake ndi atate athu, mulungu wake komanso mulungu wathu. Ndikudzera mwa iye tsopano tithakutsendera chifupi ndi mpando wa chisomo cha mulungu.


    John 20:1-18, Jesus fulfilled all that he came to do on earth. Jesus payed the ransom for our sins something that we could not do on our own. Jesus when in the tomb, God could not let his body to decay for he was righteous. So he resurrected him. Now he is in heaven with his father and our father, his God and our God. And now we can with confidence approach the throne of grace of our God.

    49 min
  • Chikondi chafika pachimake mwa ife/Love is made complete in us

    1 Yohane 4:12-21, onse okhulupirira uthenga wabwino amalumikizidwa ndi mulungu ndipo chiyanjano chawo chimakhala chenicheni. Chifukwa cha chikondi chimenechi ndi chiyanjano chimenechi timaonetsera chikondi chathu pa ena ndipo chikondi chake chimakhala choonadi. Mulungu akutilimbikitsa kufikira tsiku la chiweruzo ndi cholinga chakuti tizayime pamaso pake opanda mulandu koma kupatsidwa mphoto ya moyo wosatha.


    1 John 4:12-21, all believers who put faith in the gospel are united with God and have fellowship with him and that fellowship is real. Because of this love and fellowship we show our love to others and that love is in truth. God is encouraging us so that on the day of judgement we will stand with confidence not to be judged but to receive the gift of everlasting life.

    1 hr 6 min
  • Anapereka mzimu wake/He gave up his spirit

    Yohane 19:30, pamene Yesu anali pamtanda kusausitsa kuti apume, anayangána kumwamba kwa atate ake nati "kwatha." Chinthu china chodabwitsa chinachitika patatha izi. Pamene ife anthu tikamwalira mizimu yathu imatengedwa kwa ife. Koma Yesu anapereka mzimu wake yekha. Imfa yake imapangitsa kuthekera kati ife tikhale opanda mantha ingakhale mavuto abwera.


    John 19:30, when Jesus was at the cross gasping for air, he looked up to his father and called out it is "finished." One remarkable thing happened afterthat. When we die our spirit is taken away from us but Jesus gave up his spirit. The death of Jesus makes it possible for us that we no longer live in fear even in the face of problems.

    49 min
  • Mulungu ndi wamkulu kuposa mitima yathu/God is greater than our hearts

    1 Yohane 3:19-24, kulimbika mtima pamaso pa mulungu kumathandiza ife kuzindikira kuti tili pa choonadi ndipo timakhala okhazikika mtima pa maso pa mulungu. Ife timalandira chilichonse tipempha kwa iye, chifukwa timamvera malamulo ake ndi kuchita zimene zimamukondweretsa. Nthawi imene tichita izi; iye amakhala mwa ife ndipo ife timakhala mwa iye.


    1 John 3:19-24, as we are strong hearted and stead fast before God, we are helped to realise that we stand in truth and we are at peace within our hearts before God. we receive all that we ask from God, because we listen to him and his commands and do all that he asks of us. All the time as we do this, he lives in us and we live in him. 

    41 min
  • Chikondi pa wina ndi mnzake ndi m'choonadi/Love for one another and in truth

    1 Yohane 3:11-18, mawu awa akutikumbutsa za chikondi chathu pa wina ndi mnzake makamaka pamene ife tsono ndi ake a mulungu, chikondi chathu chisakhale cha pakamwa koma cha ntchito zathu ndi m'choonadi kuwonetsera chiyanjano chathu ndi mulungu wathu mwa ambuye wathu Yesu Khristu.


    1 John 3:11-18, these words are reminding us of our love for one another especially now that we are children of God, our love for each other should not be in words only but in works also and in truth showing our fellowship with God through our lord Jesus Christ.  

    1 hr 9 min

About Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

From the publisher's feed

Sermons and teaching in Chichewa and English

More shows like Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

Gospel Life | Malawi, Missions, and More by Josh Hutchens & Isaac Dzimbiri | Gospel Life

Gospel Life | Malawi, Missions, and More

12 Listeners