
Sign up to save your podcasts
Or


Pamene tapanga ophunzira, tiziyembekezera ophunzira atsopano kupanganganso ophunzira ochuluka. Pamene tawazindikira, tikuyenera kuwaphunzitsa komanso kuwatumiza ophunzira atsopanowa. Tikatero timakhala kuti tatumiza alimi ochulukira m’minda ku ntchito yodzala mipingo.
When we make disciples, we should expect new disciples to make more disciples. When we identify, invest in, and send out these new disciples, we send more farmers into other fields for the work of church planting.
Pamene talalikira uthenga wabwino ndikuphunzitsa okhulupirira atsopano, ndi nthawi yoti tiwakhonzekeretse okhulupirira atsopano kuti akhale mpingo. Mpingo umakhala ndi anthu omwe ndi ziwalo ndipo amasonkhana pamodzi kuti amve ulaliki wa baibulo. Mpingowo umachita ubatizo ndi mgonero wa ambuye ndipo umatsogozedwa ndi abusa ndi atumiki.
After we have preached the gospel and discipled new believers, it is time to organize the new believers into a church. A church consists of member that assemble together for biblical preaching. It practices baptism and the Lord’s Supper and is led by pastors and deacons.
Monga munda omwe wayamba kukula, akhirisitu atsopano amafunika chisamaliro chauzimu pafupipafupi. Yesu akutilamula kuti tibatize wokhulupirira atsopano ndi kuwaphunzitsa malamulo ake.
Like a field that has started to grow, new Christians need constant spiritual care. Jesus commands us to baptize new believers and to teach them his commands.
Kudzala kachisi wa tsopano kuchokera mubaibulo, tikuyenera kudzala munda ndi mbewu ya uthenga wa wabwino. Izi zimafunika kuti tifalitse uthenga wa bwino momveka bwino komanso kwa anthu ambiri. Pamene tifalitsa uthenga wa mulungu, Yesu akutiuza kuti tiyembekeze mayankho anayi (Marko 4:11-20).
To biblically plant a new church, we must sow the field with the seed of the gospel. This requires us to proclaim the gospel clearly and widely. When we proclaim the gospel, Jesus tells us to expect four different responses (Mark 4:11–20).
Timakhonza munda watsopano wodzalapo mpingo kudzera mupemphero. Timamupempha Mulungu kuti akonzekeretse nthaka yoti ilandire mbewu ya uthenga wa bwino. Koma tikuyeneranso kuzikonzekeretsa tokha popanga kafukufuku wa munda, kufunafuna munthu wamtendere, ndi kupanga ndondomeko zokaphunzitsa uthenga wabwino.
We prepare a new field for church planting through prayer. We ask God to prepare the soil to receive the seed of the gospel. But we must also prepare ourselves by researching the field, seeking a person of peace, and making plans to preach the gospel.
Cholinga chathu ndikupanga ophunzira ndipo timapanga ophunzira polalikira uthenga wabwino ndi kudzala mipingo. Kuti tidzale mpingo timayenera kukonza munda, kudzala mmunda, kusamalira munda kenaka kukolola mmunda.
Our goal is to make disciples, and we make disciples by sharing the gospel and planting churches. To plant churches, we must prepare the field, sow the field, tend the field, and then harvest the field.
Akolose 3:4; Yakobo 1:2-4. Imfa ya Yesu siikutitsimikizira kupindula. Akhirisitu amavutika. Koma kuvutika kumeneku ndi kuyesedwa kwa chikhulupiliro chawo. Iwo amene amakhulupiliradi sangataye chiphulumutso chawo konse, komano chikhulupiliro choonadi chimazindikirika pamene akhalabe okhulipirika mpaka kumapeto.
Colossians 3:4; James 1:2–4. Jesus’ death does not guarantee us prosperity. Christians suffer, but this suffering is a test of our faith. Those who truly believe can never lose their salvation, but true faith is demonstrated only by remaining faithful to the end.
Akolose 3:5-10; 1Yohane 1:5-9; Marko 7:21-23; Yakobo 1:14-15. Ana a Mulungu si a ngwiro. Amatha nthawi zina kuchimwa koma ana a Mulungu amavomereza matchimo awo ndipo amafunafuna kupha machimo awo kuchokera ku mizu po khonzanso malingaliro awo ndikuvala munthu watsopano.
Colossians 3:5–10; 1 John 1:5–9; Mark 7:21–23; James 1:14–15. Children of God are not perfect. They do sometimes sin. But Children of God confess their sins and seek to kill their sin at the root by renewing their minds and putting on the new self.
Mulungu watitsindikiza ndi Mzimu Woyera kutitsimizira kuti chipulumutso chathu ndi chamuyaya. Komanso kuti madalitso onse achipulumutso athu tizalandi kutsogolo.
Akolose 3:18–21; Yoswa 24:15; Deuteronomo 6:6–9. Pamene Mulungu anakupangani kukhala atsopano, anayamba kupanga banja lanu kukhanso latsopano. Pangani Mulungu ku khala Mulungu wa banja lanu kudzera mukupembeza kwa banja.
Colossians 3:18–21; Joshua 24:15; Deuteronomy 6:6–9. When God made you new, he began to make your family new. Make God the God of your home through family worship.
From the publisher's feed

12 Listeners