Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

Download on the App Store

Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine episodes

  • Kondani Anthu Ena | Love Others

    Akolose 3:12–13; Yohane 13:34–35. Dziko lidzadziwa kuti ndife ana aMulungu kudzera mu chikondi chathu. Baibulo likutilamulira ife kuti tikonde Mulungu, anasi utuu, wina ndi m'dzake, adani athu, komanso iwu omwe ndi osowa.

    Colossians 3:12–13; John 13:34–35. The world will know we are children of God by our love. The Bible commands us to love God, neighbor, one another, enemies, and those in need.

    28 min
  • Kuchita Umboni wa Yesu | Witness about Jesus

    Akolose 3:1–4; 4:5–6; Machitidwe 1:8. Mulungu akuyitana mKhristu wina aliyense kukhala mboni ya Yesu. Kuchitira umboni wokhudzana ndi Yesu ndi kosavunga monga kuyakhula nkhani yako ndi nkhani ya Mulungu.

    Colossians 3:1–4; 4:5–6; Acts 1:8. God calls every Christian to be a witness about Jesus. Witnessing about Jesus is as easy as telling your story and telling God's story.

    Preacher: Dr. Joshua Hutchens

    Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino | Discipleship: Living the Gospel
    Translator: Isaac Dzimbiri

    24 min
  • Perekani ku Mpingo Wanu | Give to Your Church

    Machitidwe 2:45; 2 Akorinto 9. Timapereka chifukwa Mulungu anatipatsa ife Mwana wake. Tikuyenera kukhala ndi dogosolo la kupereka kwathu komanso tikuyenera kupeka wokondwera.

    Acts 2:45; 2 Corinthians 9. We give because God gave us his Son. We need to plan our giving and to give cheerfully.

    Preacher: Dr. Joshua Hutchens

    Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino | Discipleship: Living the Gospel
    Translator: Isaac Dzimbiri

    22 min
  • Imfa, Chiwukitso komanso Mapemphero a Yesu Khristu Tsopanolingo

    Oyera mtima apirira muchikhulupiriro chawo chifukwa imfa ya Yesu yachotsa chostutsa china chilichonse komanso mlandu uliwonse otsutsana ndi sosakhidwa a Mulungu. Chiukitso cha Yesu ndi chitsimikizo cha chikhulupiriro chathu komanso mpemphero ake opemperera oyera mtima amatsimikizira kuti chikhulupiriro cho sichifowoka.

    Preacher: Isaac Dzimbiri

    Class: Kudzama Choonadi
    Series: Kupirira kwa Oyera Mtima Chikhulupiriro Chawo

    1 hr 15 min
  • Sonkhani Pamodzi kuti Mupembeze | Gather for Worship

    Machitidwe 2:42; Ahebri 10:24–25. Timasokhana pamodzi kuti tipembeze ndi cholinga choti tithandizone wina ndi nzake kukula musinkhu mwa Khristu. Tikuyenera kukhala ndi chikhalidwe chopembera ndi mpingo umodzi nthawi zonse.


    Acts 2:42; Hebrews 10:24–25. We gather to worship to help one another grow to maturity in Christ. We must make worship with our church a habit.

    Preacher: Dr. Joshua Hutchens

    Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino | Discipleship: Living the Gospel
    Translator: Isaac Dzimbiri

    31 min
  • Werenga Baibulo | Read the Bible

    Machitidwe 2:42; 2 Timoteyo 3:16–17. Kudzera mukuwerenga Baibulo, timamva Mulungu akuyakhula nafe. Khalani ndi dogosolo lakawerenge ka Baibulo komanso yambani kuwerenga.

    Konzekerani Kuwerenga Baibulo: https://chiphunzitsochoona.com/wp-content/uploads/2020/05/Bible-Reading-Plan-Chichewa.pdf

    Acts 2:42; 2 Timothy 3:16-17. By reading the Bible, we hear God speak to us. Have a plan for reading the Bible, and get started.

    Bible Reading Plan: https://chiphunzitsochoona.com/wp-content/uploads/2020/05/Bible-Reading-Plan-English.pdf

    Preacher: Dr. Joshua Hutchens

    Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino | Discipleship: Living the Gospel
    Translator: Isaac Dzimbiri

    31 min
  • Yambani Kupemphera | Start Praying

    Kudzera mupemphero, timamva umwana wathu mubanja la Mulungu. Yesu anatiphuzitsa momwe tikuyenerera kupemphera munjira yomwe ikuyenerera ku pereka ulemerero kwa Mulungu.

    Through prayer, we experience our adoption into God's family. Jesus taught us how to pray in a way that glorifies God.

    Preacher: Dr. Joshua Hutchens

    Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino | Discipleship: Living the Gospel
    Translator: Isaac Dzimbiri

    44 min
  • Mphamvu za Mulungu Zosunga Oyera Mtima

    Chifukwa cha mphamvu za Mulungu ndi chifuniro chake, anthu woyera mtima apirira mu chikulupirira chawo mpaka kumapeto kwa moyo.

    Preacher: Isaac Dzimbiri

    Class: Kudzama Choonadi
    Series: Kupirira kwa Oyera Mtima Chikhulupiriro Chawo

    50 min
  • Batizidwani | Be Baptized

    Ubatizo ndi njira yoyambirira ya kumvera monga mKhristu watsopano. Uma onetsera kwa aliyense yemwe alikunja zomwe Mulungu wachita kuti mwa munthu.

    Baptism is your first step of obedience as a new Christian. It is the public sign of your faith. It shows to everyone outside what God has done inside.

    Preacher: Dr. Joshua Hutchens

    Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino | Discipleship: Living the Gospel
    Translator: Isaac Dzimbiri

    27 min
  • Uthenga Wabwino ndi Mphamvu ya Mulungu | The Gospel is the Power of God

    Aroma 1:16–17. Uthenga Wabwino ndi mphamvu ya Mulungu yopulumutsa chifukwa mu Uthenga Wabwino mphatso ya Mulungu ya chilungamo ya onetsedwa.

    Romans 1:16–17. The gospel is the power of God for salvation because in the gospel God's gift of righteousness is revealed.

    Preacher: Dr. Joshua Hutchens

    Class: Kuyenda m'Choonadi | Walking in Truth
    Series: Aroma | Romans
    Translator: Isaac Dzimbiri

    32 min

About Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

From the publisher's feed

Sermons and teaching in Chichewa and English

More shows like Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

Gospel Life | Malawi, Missions, and More by Josh Hutchens & Isaac Dzimbiri | Gospel Life

Gospel Life | Malawi, Missions, and More

12 Listeners